:Writings Speak
  Non - Arabic Articles Nayanga/Chichewa

: Writings Speak
: webmaster

 

Anti Ahmadiyya Mouvement in Islam

 

KAMBA MOLEMBA

KUBADWA KWA MIRZA GHULAM

CHIYAMBI CHA UMOYO WA MIRZA QADIANI

 

« Ndina badwa mchaka cha 1839 kapena 1840 A.D ndinali umodzi wa ana amapasa.

Wina mwaine anali mkadzi dzinalache ndi Jannat (paradiso). Mkati mwa malemba akuti

« Ya adam uskun antaa wa zaujoka al-jannah, » zomwe zinavumbulutsidwa mu

Braheen Ahmadiyya tsamba la 496 zaka 20 zapita, mau akuti « Jannat » adatenga malo

aku ulu kotelo kuti mapasa wamkadzi adapasidwa zinalo, ndipo uyu mapasa anafa ali ndi

miyezi 7 ». (
Tiryaq-ul-quloob, roohani kazain vol. 15 Tsamba la 479 olemba Mirza

Ghulam Ahmad Qadiani).

« Bambo wanga ndi Mirza Ghulam khazain, anali ndi chuma ndipo otchuuka. Onyamata

wanga ndi naphudzila ndili ndizaka 6 – 7 ndi mphunzisi waku Persian omwe adapatsidwa

kuti andi phyzise qurran monga wa nchito ndi ma book ya lilime la persian. Dzina la

mphutsi ndi fazl llahi. Nditafika dzaka 10 khumi, ana pezeka wina mphuzitsi wachiarab

omwe ndi moulvi, kuti naeso andi phuzise, dzinalache ndi Fazl Ahmad. Pomwe ndinali

ndi zaka 17 – 18, ndina pitiliza maphuzilo kuchokela kwa a bambo anga. Ndi napata

maphuzilo a grammer, logic ndi hikmat (medicine) ndi ena ma buuku a medicine ku

phuzisidwa ndi a abambo anga. Chi*****wa cho fooka kwa nthanzi, abambo anga

ankandiletsa kuwelenga ko pitilira malile.

« Nthawi yomwe azuungu achi Britishi adalanda mudzi wathu, abambo anga ada

mangala ku khoti ya azuungu kuti ababwezele. Ni dakhala ndi mpata oima kuimilira

mulandu omweuyu. Ngakhale zinali zo nditangwanisa umoyo wanga ndiponso sindi

nafune kuti ndipitilize umoyo wanga pamalo monga awa apamudzi, koma ndi

dakakamizidwa kuionela mudzi ndi zina zofunikila momwemo. Pomwepo ndinali

kugwila nchito ndi azuungu achi british government zaka zo chepa ku Sialkot khoti

monga kalembela malipilo ya Rs. 15/- pa mwezi.

« Sipanapite masiku ambiri ndi nasiya nchito ndi nabwerela ku Nkhani zaku mudzi.

Nthawi ndinali kuganiza thandauzo la buuku la Quran (tafseer). Pomwe ndinafika zaka

30 – 35 abambo anga adamwarila, zidandifikira zimwetumwetu zolankhula ndi

Mulungu (Mukalimat-e-llahiah) kopanda marile ».

(Kitab-ul-bariayh pp. 134 – 136 ndemanga Mirza Ghulam Ahmad Qadiani, Roohani

Khazain vol. 13 page 180, Tuzuk-E-Ahmadi yolembedwa ndi Akhbar-al-hakam Qadiani

yochu uka nambala vol. 37 nambala 18519 tsikula 21 – 28 May 1934 A.D).

MIRZA AKOKEDWA NDI NDALAMA ZA PENSHIONI.

 

« Bismillah ar-rahman ar-raheem. Hazarat waalida sahiba (olemekezeka amai akazi a

Mirza Ghulam) anati kwaine, nthawi ina ndikali mnyamata, pomwe Hazat Masseh

Mowood anapita ukatenga ndalama za ambuye ako za penshioni, a Mirza Imamdeen

(muphwa wa Mirza Ghulam) ada londola iye ukatenga makhobili.

Koma nthani yomwe yotenga ndalama za penshioni anaona kuti zina zachesizili bwino ai

koma anamatenga (Mirza) mmalo mwa Qadiani, adazweta nayeapa ndi apa mpaka

momwe ndalama zija zitatha, ndipo imamdeen anaona kuti zinthu sizili bwino pomwepo

ana thawira malo ena ndikumsiya ekha. Hazarat Maseeh Mowood zidamvuta kuti

abwelele kunyumba chi*****wa chakuti ndalama zonse zidatha anamva manyazi chi*****wa

ambuye ache anamfunitsitsa kuti abwelele pa nchito, komabe adayamba nchito kukhoti

kwa achiwili wa comishiona boma ya Sialkoti kwa malipilo yochepa”.

(
Seeratul mahdi part 1 page 41 yolembedwa ndi Mirza Basher Ahmad mwana wa Mirza

Basher Ahmad mwana wa Mirza Ghulam).

BANJA LA CHEEPA

Bambo wanga, Mirza Ghulam Murtuza, adakondetsetsa mpando wo khalapo kwa nduna

Darbar, anali mmodzi wachilakolako ofunila mafuno abwino a British Government ndipo

olimba mtima, koti nthawi ya chiwawa mu chaka cha 1857 A.D ankathandizila kwabasi

ufumu wa azungu ndi Boma lao, kotelokuti ada kwanisa ku gula 50 mahachi kuchosa

ndalama zake ndi kupeleka othandizila asilikali 50. Koma ufumu wa Mirza Ghulam

ndimapatoache anayamba kuchepekela tsiku ndi tsiku koti matsiku athu ndi banja ai

linayamba ku chepekela anthu adatha”.
(Tohfa-e-qaiser, roohani khazain vol. 12 tsama

270-271).

“Zotuluka umo azuungu achi british adalanda zonse pamodzi ndi thaaka yomwe

pambuyo pake anati tikupatsani penshioni ya Rs, 700/-yokha pa chaka, kenaka nu

bwezaso ndalama zochepa Rs, 180/ - nthawi atamwalira ambuye anga kenaka azuunga

anati uchokela lelo taima kupeleka ndalama kulibe chanu kumalo anuwa, izi zonse

zinadza nthawi amalume anga anamwalira (akuulu a atate) atamwalira. (
Seerat-ul-Mahdi

part 1 page 41 olemba Mirza Basher Ahmad mwana wa Mirza Ghulam Ahmad Qadiani).

MATENDA KWA OSANKHIDWA UYO (AKUTELO).

“Mano a Mirza Ghulam Ahmad Qadiani adali owora kotelo kuti anali kupweteka

koopsya kotelokuti chi*****wa chaicho mmimba munadza matenda ama Ulcer ndiposo

lilime lache naloso linali ndi matenda ama Ulcer. (
Seerat-ul-mahdi part 2 tsamba 135

olemba Mirza Basher Ahmad mwana wa Mirza Ghulam Ahmad Qadiani). Lilime linali

ku chosa mafina oopsya.

“Tsiku lina aba akuulu anagwa pa dzene ndi kuvulala koopsya kotelokuti dzanja lama

dzele ai lidathyoka, kotelo kuti dzanja lija silinagwirepo nchito inailiyense mpakana

mmanda”.

(Seeratul-mahdi part 2 tsamba 198).

KHUNYU (CHINYULUNYULU) KHUNYU

 

Taonani osankhidwayo akupezeka ofoka ku ubongo, kwathawi yaitari asana peze

banja. Ndidadziwakuti ndili ndimatenda a khunyu”.

(Kalata wa Mirza Ghulam Ahmad Qadiani tsiku la 22 – 02-1887 mu buuku ya

Maktoobate Ahmadiyya vol. 5 tsamba 14 kuchokela buuku la Navishta-e-Ghaib olemba

Khalid Wazirabadi).

Nthawi itafika yopeza banja mtima ndi ubongo zonse zina li zofooka ndiposo

ndinali kunva chizwezwe zosezi zidandi kakamila nthawi yaitali; chi*****wa chaichi

sindinali kupumabwino ai (osa sangalala umoyo onse) chi*****wa chamanganizo

(kupenga) ndikusowa chilakolako cho kumana ndi mkadzi mpanvu za umuna

ndilibe”

(Tiryaq-ul-Quloob Roohani khazain vol. 15 tsamba 203 olemba Mirza Ghulam Ahmad

Qadiani).

KALATA KWA HAKEEM NOORUDDIN, MIRZA ANATI:

Ineyo nda chilitsidwa ndi mankhwara yako unandipatsa. Ang’ono mwamatenda

monga khunyu ndi mphanvu zaumuna (Lethargy) ndi utuupa mimba (Gastric

Acidity) ai ndapola ndiku chiila. Chi*****wa chaicho nidali ndi matenda oopsya

kotelokuti madzi achimuna sanali kutuluka nthawi yokumana ndi mkadzi wanga

kenaka ndi kagona mkodzo utuluka okha. Kuchepekela mpahvu zokomana ndi

mkadzi chikufwa cha matenda omweo. Chi*****wa chaicho mankhawala ako

unandipatsa aja ai ndi kwanisa ku gwira nchito yokumana ndi mkadzi mphavu

zabwerela.

(MAKTOOBAT-E-AHMADIYYA VOL. 5 NO. 2 OSONKHANISA MA KALATA NDI

MIRZA GHULAM AHMAD QADIANI).

Chibvumbulutso chi chabwela chi*****wa cha ukwati, nthawi iyo mtima wanga ndi

ubongo ndi thupi zinali zo fooka koma kuchotsela matenda a Diabetes Mellitus ndi

matenda a chizungulire (Dizness) mmutu ndi kukhala osakondwa wamadandaulo

amtima (Depression), ndina dziwa kuti ai ndiliso ndi chifuwa chamidulo

(Tuberculosis) mwa ine.

(Nuzool-e-Maseeh, Roohani Khazain vol. 18 tsamba 587 umboni ndi Mirza Ghulam

Ahmad Qadiani).

Iyeyu Mirza Ghulam Ahmad Qadiani anali wachidule kumanga Ramadan osa

kwanilisa mwezi wa Ramadan kenaka anali kulipila masiku ena popasa anthu

mwina malipiro; chi*****wa chaicho ndi matenda ake anali kugwidwa ndi khunyu

ngakhale mmwezi wa Ramadan kenaka anagwidwa ndi kumasula panthawi ya

Magrib (dzuwa litalowa). Anali akulu awa akugwidwa ndi khunyu nthawi ndi

nthawi kotelokuti umoyo wao unali mchiopsyezo kweni kweni”.

(Seerat-ul-Mahdi part 1 tsamba 51 olemba Mirza Ghulam Ahmad Qadiani).

Hazart Sahed anali ndi matenda odetsedwa achimdulo (Chronic Melancholic).

Matenda aya ndi akatengela apabanja. (Mirza Sahib sangakhale kapena kugwira

nchito ya uneneri – olemba). Mirza sahab anali ndi amalume ache (mbanja) dzina

lache anali Mirza Jamiat Baig. Anali ndi mwana wa mwamuna umodzi ndi mkadzi

umodzi ndipo osewa anali ndi matenda a misala kubongo. Mwana wa mwamuna

dzina lache ndi Mirza Sher Ali, mwana mkadzi anali Hurmat Bibi. Omwe ada

manga banja ndi Hazrat Sahab”.
(Mirza ndi Hurmat Bibi – osewa anali ndimatenda ya

misala!! Zamanyazi kwabasi ! nanga ana atabadwa akhala otani ? zodabwitsa kwa basi

– olemba). (Seerat-ul-Mahdi part 1 tsamba 51).

KHUNYU (MELANCH EHOLIA) MBILI YAKALE NDI MANKHWALA.

Matenda amaganizo ndi khunyu ndi amodzi matenda akale kale chiyambi cha munthu

pano padziko la pansi. Anga khale mmalemba akale zonsezi zilimo monga matenda

aubongo. Olemba akale anaikamifano chimodzi modzi zaaka zapita 2,000 ufikila 4,000

mpkana lelo.

Anga khale anthu aku Greek adalemba mdodnomeko wamatenda aya aubongo. Koma

2,300 zaaka zapita, matenda awa ozelezeka a (Psychiatric) mabvuto awa ndi ochokela

monga achifuniro o sati achilengedwe (capriciousness). 1zozo za matenda aubongo

(Psychiatric) nalero akalipobe. Makhate ndi khunyu (epilepsy), uzelezeka (Mania)

khunyu (Melancholia) ndi (Paranoia). Olemba akuti mkadzi omwe ali ndi khunyu

kapena khunyu sa mapeza turo, chakudya osakoma, angakhale lero lino zikadalipo be

(Depression).

Nthawi ya ulamuliro wa Aroma, sing’anga Galen molemba anati kumatendawa a

(Depression) ambiri odwala amaoneka a mantha, osokonezeka, osadziwa za umoyo wao

ndiponso odana ndi anthu. Mosimikiza zonsezi zimapedzeka ku ubongo zomwe zima

gwira mizipe, ndipo munthu kukhala ozelezeka monga odwala (Melancholia) mutuwake.

Akupitiliza Galen kuti munthu otele wa (Dyshmia) amakhala okwiya mwamsanga

(Crasis) ndi ponso ofooka (Chymos).

Robert Borton “kaswili wa” (Anatony of Melancholia) ananena ndi ku ulusa chaka cha

1630, mofotokoza mdondomeko bwino anati (Melancholy) “ndi matenda omwe

amagwira muutu ndi ubongo” nthawi ndi nthawi mo onjezera uwawa ndipo maganizo.

Burton ndiye anadzetsa chibvumbulutso kuti mankhwala amakono akhale odzwa kuti

misaala imabwera bwanji, ndiye ichi ndiye chi*****wa cha ubongo (Depression), kenaka,

uzungulira kwa muutu ndi kukhala wa manyazi, openga, okwiya, osafuna kukomana ndi

mkadzi malo amodzi.

Wina wache kaswiri wa dzina la Freud adalemba mbuuku lache (mourning and

Melancholia) lolembedwa mchaka cha 1917. Anati kulemba Freud (Melancholia), ndi

matenda omwe amapanga munthu ukhala oopa kathu kenache kalikonse monga openga

kapena odabwa ataona kanthu.

Ndiponso (Delusional Depression) yatsimikidzidwa kuti umakanika iwe wekha kukhutira

chili chonse kenaka umakhala ozazuka. Zanveka kuti amisala wa amakhala okwiya,

openga, ozazuka ngati wina wache akunena kapena kulankhula, monga mkadzi akati

tiyeni tikomane za chikwati ama zazuka chi*****wa chila kolako alibe chokumana ndi

 

mkadzi. Aganizani, taonani zotelezi zingapedzeke kumunthu omwe ali mneneri (Mirza)?

Bwenzi freud ankadziwa akada werenga naeso zauyu Mirza.

Uzelezeka, upenga anthu-anatulukila matendawa kalekale zikwi ndi zikwi zaaka zapitazi.

Oyamba ndi (Philosopher) kenaka asing’anga madotoro. Ufikira lelolino ai zafalitsidwa

pose pose mvipatala ndi madotoro akudziwa bwino zamatenda amisala.

“Ulingana ndi Hikmat ndi Greek mmalamulo awo akuti, matenda awa amabwera

chi*****wa cho chulukira kwa (Black Acidic) mmimba. Kalikonse kamthupi kakagwidwa

ndi Black Acidic kamapangitsa chakudya mmimba ndiposo mmvuche oipa osatuluka,

umapita ku ubongo. Zikatero, zima sanduka ma (Symptoms): odzadzamwa (Anoxia)

chi*****wa matumbo mmimba salibwino ai, chakudya osagaidwa bwino, usegula mmimba

apa ndi apa, kuiwala iwala, kugeya konunkha uchokera mmimba. (kodi mnneri monga

Mirza angakhale ndi umoyo otero?) kalembera akufusa.

(
Chionesero chachiyambi cha matenda oopya monga amisalaku ubongo. Olemba

Allamba Burhanuddin Nafeesa).

« Zanveka kuti matenda a (Melancholia) ndi zotulukamo, chi*****wa cho lephera upanga

zachikwati ndimkadzi chi*****wa chakuti matendawa amayambira ku (Liver) ndi mmimba.

Koma lero lino, ndi chodziwika kuti ndi matenda amisala monga (Hysteria) kwa azimai.

Chiyambi ndi mmimba ndiye momwe mudzetsa zosezi ukhala ofooka maganizo

(Meloncholia) kwa a zibambo. Chidzindikiro :- odwala openga, maganizo amaganiza

zaiye yekha, kenaka kumati ine ndine ndi chita ichi ndiichi nthawi ndi

nthawi…………………………osafuna kudya, kuvutikila kuchotsa chimbuzi ».

(Makhzan-e-Hikmat, olemba Hakeem Dr. Ghulam Jeelani).

“Kusowewa kupnga chimbudzi, kusegula mmimba (Sailorhea) utuupa mimba

(Borbarygmi), kupsya mmimba, osakoma chakudya, mpweyaoipa uchokera mmimba

upita kumutu, zosezi ziletsa upita ku chimbudzi ndi chakudya, kenaka utentha mamba ndi

thupi, manja ndi miyendo kenaka ku dzidzira kwa thupi kambiri mibiri thupi limafooka,

kambiri maso amawawa, kulema kwazikope, kutentha kwa mutu ndi ubongo, kupweteka

ka mutu zosezi ndi chi*****wa chamatenda akhunyu (Melancholia)”.

(Akseer-e-Azam vol. 1 tsamba 189 olemba Hakeem Muhammad Azam khan).

Mwawerenga zonsezi kulingana ndi nkhani za matenda. Mwapatsidwa mpata nonse kuti

muganize bwino zomwe ozicha kuti ndine mneneri (Mirza) omwe alankhula ndi

Mulungu apezeka ndi matenda monga tanenawa oopsya akhunyu ndi khunyu kumanama

anthu kuti ndine (Messaya) omwe apezeka ndi nthenda ya ( melancholic), anga itandidwe

bwanji kuti ndi mtumiki? Utamusatila mneneri monga uyu kodi ungakhale iweyo

musilam okwana? Musaike chikhulupiliro ndi kukhala okulupilira monga aneneri

onyenga, pokhapo mneneri oma liza iyeyundi mtumiki (Muhammad) S.A.W.

Mtumiki Muhammad (S.A.W) akuti:

“Otsatira aine tanvani, azapezeka aneneri onyenga okwana 30 aliyense mwaiwo onama

amati ndatumidwa ndi Mulungu monga mneneri. Ndi kwainu nonse kudziwa kuti

 

mneneri onyenga uyu ndani kodi chiwerengero chache ndi chotani? Tsopano tiyeni tione

anzeru zakuya monga akalembera akunena zamatenda a (Melancholia) akhunyu,

kalembela wina monga Hakeem akuti:-

ABU ALI SENA AKUTI:-

“Matenda a (Melancholia) ama mphanga munthu ukhala openga kumalankhula zo

bwebweta bwebweta kumaziganinizira monga ndi munthu weniweni kumaziika

pamtengo wapatali. Akagwidwa ndi khunyu kapena khunyu amanva chidima pamaso

ubongo naonso uma sokonezeka kenaka odwara uja amapenga monga ufuntha chi*****wa

chamdima akagwidwa ndi matenda wa. Kambiri (Liver) mphafa imatentha, amati

matenda a (Hypochonriasis). Chakudya ndi madzi zikalowa mmimba zimakhala zakuda

kapena (blackish) mmimba muja zimatupisa mimba kenaka mphweya umatengedwa

upita ku ubongo, izozo zimapanga (Gaseous Melancholia) ukhala openga nthawi ndi

nthawi”.

(Canon in Medicine, Fun-E-Awwal book ya 3, Abu Ali Sena).

Kachilitsidwe: ndikofunikira munthu odwala (Melancholia) akhale otangwanika ndi

zinchito izi ndi izi ndi kuti mtima wake upuume bwino ndiposo akhale pafupi ndi anthu

omwe azamnama kuti ndinu nokha ndinu nokha kuti iye yo odwala uja azikhala

okondwera kenaka usakuikamozako ndiviinyu (Wine) kuti odwala uja akhale osangalala

ataledzera pangono”.

(Canon in Medicine olembe ndi Aviecnia).

Dziwa: Mirza Ghulam Ahmad Qadiani anali kumwa mowa (Wine) ndi mapilisi

oledzeletsa (Opium) chi*****wa cha matenda ache.

“(Melancholia) ayandi matenda omwe amasokoneza maganizo abwino kukhala openga

ngati wamisala chi*****wa samakhala munthu okwana ai”.

Kambirimbiri odwala amakhala munthu okamba kamba zinthu zopanda pache kenaka ndi

kumalodzela zomwe zolota kuti zaku tsogolo zikhala motele motele zabodza basi.

Kenaka imafika nthawi yakuti amanena kuti iyeyo ndimgero”.

(
Guide to the Aetiology ndi chiyambi chamatenda ya Melancholia olemba ndi Allama

Burhanuddin Nafees).

Zosezi zamatenda awa ndi zotulukamo zimadza momwe takambila pachiyambipo

chi*****wa cha umoyo wa munthu. Mfano, ngati munthu wa chikhulupiliro omwe

wamisala angaziche iyo mneneri ndi kuonetsa zodabwitsa (Miracles) ofuntha kuma

lankhula mau aulariki ndi chipulumutso kuanthu, zitheka bwanji munthu openga

oteroyu?”

(Akseer-e-Azam vol. 1 tsama la 188 olemba ndi Muhammad Azam Khan).

“Odzicha iyeyo mneneri, ngati nizoona bwanji adwara matenda a misala (Hysteria)

monga kupenga (Melancholia) kapena khunyu (Epilepsy), ichi ndiye chidzindikiro

chakuti iyeyu sanga khale mneneri ai, chi*****wa izi zonse zimampangisa iyeyo mneneri

onyenga ukhala ndithu onyenga kapena onama alibe chiyambi ai”.

 

(
Slemba ndi Dr. shahanawaz Qadiani mu Magazine ya onani chipembezo, Qadiani tsiku

August 1926 A.D).

Mirza Qadiani ndi mowa + uledzera (Drug ndiye mkhlidwe wache.

“(Opium) zidonge ndi mapilisi oledzeletsa zimapendzeka kumunthu odwara misala

(Hazrat Maseeh Mirza Ghulam Ahmad Qadiani) amanena kuti mapilisi oledzeletsa kwa a

dotoro ake, (Opium) ndi amodzi omwe andi chiritsa ine. Chomwechi (Opium) pamodzi

ndi mankhwara ena amachilitsa ndipo uledzera nakoso ndichimodzimodzi nazonso zima

chilitsa. Chi*****wa wina wache mwaife nthawi ina ana mwapo (Opium).

“Hazrat Maseeh Mawood onyenga mneneri Mirza Ghulam Ahmad Qadiani adalonjedza

kuti mankhwara (Tiryaq –E-Llahi kuti (Opium) ndi mankhwala ochokera kwa Mulungu.

Kambiri aya mankhwala ana mpatsa kumwa uyu mneneri onyenga Hazrat Khalifa

oyamba – Hakeem Noorud Din olemba Hazrat (Mirza Qadiani) anali kumwa mneneri

onama uyu miyezi 6, nayenso akagwidwa ndi khunyu naenso anali kumwa (Opium)”.

(
Article olemba ndi Mian Mahmood Ahmad khalifa Qadiani mbuukula Akber Al Fazal,

Qadian vol. 17 no. 6 pa 19th July 1929).

Vinyu (Tonic Wine):-

“Kwa okondedwa mbale Muhammad Hussein Sahib Mulungu akudalitse. Assalam-oalaikum

Chiyambi iwe mohammad watumidwa lero. Zipangizo ziri tayari. Funafuna zipangizo

zako botoro limodzi la vinyu (Tonic Wine) uchokera musitolo La Plommer koma ndifuna

botolo la vinyu (Tonic Wine) sunga mmutu wako. Zose ziri bwino.

(osaina: Mirza Ghulam Ahmad Qadiani).

(
Makalata a Imam kwa P. S. Olemba Mirza Ghulam Ahmad Qadiani upita kwa Hakem

Mohammad Husain Qadiani, mwini wa chipatala Rafiq-us-sahat Lahore Pakistan).

Choonadi cha vinyu (Tonic Wine) amaguula kusitoro la Plommer boma la Lahore

Pakistan umboni opitira mwa Dr. Aziz Ahmad anati polemba:-

Ndalamulidwa kuti ndizigula mowa uyu wa vinyu (Tonic Wine) mustitoro la Plommer,

adayankha nati:

Vinyu (Tonic Wine) ndi mowa oledzeletsa oopsya omwe umagulidwa ndi maiko akunja

monga ku (U.K) muma botoro otsekedwa bwino bwino. Mtengo wache ndi R.S. Annas 8

(1-09-1933)”.

(Sauda-e-Mirza tsamba 39 olemba Hakeem Muhammad Ali, mkulu wasukulu ya Tibbiya

boma la Amratsar).

Taonani pangwe ngwengwe mneneri onyenga zomwe za turukamo kuti Mirza Ghulam

Ahmad Qadiani saku kwana ai kukhala mneneri, kapena kukhala uja olengezedwa monga

(Mahdi) mwina monga mphulumutsi ai, mpulumutsi sanga khale ndi matenda a khunyu,

misala, ozelezeka sizingatheke oteleyo woledzera alankhulane ndi Mulungu ai. Kenaka

kwaturuka onyengayu akumwa (Opium) ndi mowa ai sakwana pa uneneri. Tiyeni

timpemphe Mulungu ati onetse njira ya chilungamo ndi kudzindikira kuti tionetsetse

aupandu awa a Qadiani naonso atsatire choonadi cha chipembezo cha mtumiki wathu

omalidza Muhammad (S.A.W). Zikanga kuti atsatire chilungama cha choonadi ndi

kumatsatira anthu a chinyulunyulu, akhunyu, amisala (Melancholiac Prophet) naonso

azakhala chimodzi modzi monga mneneri wao onyenga ndiposo chipembezo chaocho

chikhala chonyenga dziwani kuti moto wa Jahena udikhira anthu onyenga.

END

Translated from English to Nyanja by :

OLEMBA NDINE SHEIKH ASSADULLAH MWALE

MUFTI OF ZAMBIA

P. O. BOX FW 306

LUSAKA – ZAMBIA

CELL: +260 97 7493870

EMAIL: assadullahmwale@yahoo.com

Anti Ahmadiyya Movement in Islam

Dr Syed Rashid Ali

P.O.Box 11560 Dibba Al Fujairah

United Arab Emirates.

E-mail: rasyed@emirates.net.ae / alhafeez.org/rashid

:   admin       (   )
: 0 /5 ( 0 )

: 26-11-2009

: 2127